Genesis 21:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Abrahamu anamdula mwana wace wamwamuna Isake pamene anali wa masiku ace asanu ndi atatu, monga Mulungu anamlamulira iye.

Genesis 21

Genesis 21:1-11