Genesis 21:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ananka nakhala pansi popenyana naye patari, monga pakugwa mubvi: cifukwa anati, Ndisaone kufa kwa mwana. Ndipo anakhala popenyana naye, nakweza mau ace nalira,

Genesis 21

Genesis 21:8-20