Genesis 2:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova Mulungu anameretsa m'nthaka mitengo yonse yokoma m'maso ndi yabwino kudya; ndiponso mtengo wa moyo pakati pa mundapo, ndi mtengo wakudziwitsa zabwino ndi zoipa.

Genesis 2

Genesis 2:1-15