Genesis 2:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova Mulungu anaumba munthu ndi dothi lapansi, nauzira mpweya wa moyo m'mphuno mwace; munthuyo nakhala wamoyo.

Genesis 2

Genesis 2:2-8