Genesis 2:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Imeneyo ndiyo mibadwo yao ya zakumwamba ndi dziko lapansi, pamene zinalengedwa, tsiku lomwe Yehova Mulungu anapanga dziko lapansi ndi zakumwamba.

Genesis 2

Genesis 2:3-12