Genesis 2:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma mtengo wakudziwitsa zabwino ndi zoipa, usadye umenewo; cifukwa tsiku lomwe udzadya umenewo udzafa ndithu.

Genesis 2

Genesis 2:13-20