Genesis 19:36-38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

36. Ndipo ana akazi awiri a Loti anali ndi pakati pa atate wao.

37. Woyamba ndipo anabala mwana wamwamona, namcha dzina lace. Moabu; yemweyo ndi atate wa Amoabu kufikira lero.

38. Wamng'ono ndipo anabala mwana wamwamuna, namcha dzina lace Benammi; yemweyo ndi atate wa Aamoni kufikira lero.

Genesis 19