Genesis 19:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo anayang'anira ku Sodomu ndi ku Gomora ndi ku dziko lonse la cigwa, ndipo anapenya, taonanitu, utsi wa dzikolo unakwera, monga utsi wa ng'anjo.

Genesis 19

Genesis 19:26-31