Genesis 19:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali pamene anawaturutsa iwo kunja, anati, Tapulumuka ndi moyo wako; usaceuke, usakhale pacigwa pali ponse; thawira kuphiri, kuti unganyeke.

Genesis 19

Genesis 19:7-25