Genesis 19:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene kunaca, amithengawo anafulumiza Loti, nati, Uka, tenga mkazi wako, ndi ana ako akazi awiri amene ali kunowa, kuti munganyeke m'mphulupulu ya mudzi.

Genesis 19

Genesis 19:8-20