Genesis 19:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu aja anati kwa Loti, Kodi muli nao ena pano? Mkamwini, ndi ana ako amuna, ndi ana ako akazi, ndi onse ali nao m'mudzi muno, uturuke nao m'malo muno:

Genesis 19

Genesis 19:7-19