Genesis 18:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati, Taonanitu, ndadziyesera kunena kwa Ambuye: kapena akapezedwa makumi awiri m'menemo. Ndipo anati, Sindidzacita cifukwa ca makumi awiri.

Genesis 18

Genesis 18:22-33