Genesis 18:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ananenanso kwa iye nati, Kapena akapezedwa makumi anai m'menemo. Ndipo anati, Sindidzacita cifukwa ca makumi anai.

Genesis 18

Genesis 18:27-33