Genesis 18:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati Yehova, Ndikapeza m'Sodomu olungama makumi asanu m'kati mwa mudzi, ndidzasiya malo onse cifukwa ca iwo.

Genesis 18

Genesis 18:18-33