Genesis 18:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati, Ndidzabwera kwa iwe ndithu pakufika nyengo yace; taonani Sara mkazi wako adzakhala ndi mwana wamwamuna. Ndipo Sara anamva pakhomo pa hema amene anali pambuyo pace.

Genesis 18

Genesis 18:8-12