Genesis 17:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

A masiku asanu ndi atatu azidulidwa mwa inu, ana amuna onse m'mibadwo mwanu, amene abadwa m'nyumba ndi amene agulidwa ndi ndalama kwa alendo ali onse, wosakhala mwa mbeu zako.

Genesis 17

Genesis 17:2-19