Genesis 16:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mthenga wa Yehova anati kwa iye, Taona, uli ndi pakati, ndipo udzabala mwana wamwamuna; nudzamucha dzina lace Ismayeli; cifukwa Yehova anamva kusauka kwako.

Genesis 16

Genesis 16:6-16