Genesis 15:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati kwa iye, Kanditengere Ine ng'ombe yaikazi ya zaka zitatu, ndi mbuzi yaikazi ya zaka zitatu, ndi tonde wa zaka zitatu, ndi njiwa, ndi bunda.

Genesis 15

Genesis 15:7-19