Genesis 15:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsiku lomwelo Yehova anapangana cipangano ndi Abramu, nati, Ndidzapatsa mbeu zako dziko ili, kuyambira pa nyanja ya Aigupto kufikira pa nyanja yaikuru, nyanja ya Firate:

Genesis 15

Genesis 15:11-19