Genesis 15:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati kwa Abramu, Dziwitsa ndithu kuti mbeu zako zidzakhala alendo m'dziko la eni, nizidzatumikira iwo, ndipo iwo adzasautsa izo zaka mazana anai;

Genesis 15

Genesis 15:4-19