Genesis 14:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaturuka mfumu ya Sodomu, ndi ya Gomora, ndi mfumu ya Adima, ndi mfumu ya Zeboimu, ndi mfumu ya Bela (kumeneko ndi ku Zoari) ndipo anawathira nkhondo m'cigwa ca Sidimu

Genesis 14

Genesis 14:5-18