Genesis 14:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma cokhaci anadya anyamata, ndi gawo lao la anthu amene ananka pamodzi ndi ine, Aneri, Esikolo, ndi Mamre, iwo atenge gawo lao.

Genesis 14

Genesis 14:17-24