Genesis 14:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anadzigawanizira iwo usiku, iye ndi anyamata ace, nawakantha, nawapitikitsa kufikira ku Hoba, ndiko ku dzanja lamanzere la ku Damasiko.

Genesis 14

Genesis 14:8-18