Genesis 13:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo dziko silinathe kuwakwanira iwo, kuti akhale pamodzi: cifukwa kuti cuma cao cinali cambiri, ndipo sanathe kukhala pamodzi.

Genesis 13

Genesis 13:1-13