Genesis 13:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzayesa mbeu yako monga pfumbi lapansi: cotere kuti ngati munthu angathe kuwerenga pfumbi lapansi, comweconso mbeu yako idzawerengedwa.

Genesis 13

Genesis 13:10-18