Genesis 12:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anamuka Abramu monga Yehova ananena kwa iye, ndipo Loti anamuka pamodzi naye: ndipo Abramu anali wa zaka makumi asanu ndi awiri kudza zisanu, pamene anaturuka m'Harana.

Genesis 12

Genesis 12:1-13