Genesis 12:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akaronga ace a Farao anamuona iye, namyamikira iye kwa Farao; ndipo anamuka ndi mkazi kunyumba kwace kwa Farao.

Genesis 12

Genesis 12:11-20