Genesis 12:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Uzikanenatu, kuti iwe ndiwe mlongo wanga: kuti cidzakhala cabwino ndi ine, cifukwa ca iwe, ndi kuti moyo wanga usungike ndi iwe.

Genesis 12

Genesis 12:10-16