Genesis 11:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo Aripakasadi anakhala ndi moyo zaka mazana anai kudza zitatu, atabala Sela, nabala ana amuna ndi akazi.

Genesis 11

Genesis 11:9-15