Genesis 10:27-31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

27. ndi Hadorimu ndi Uzali, ndi Dikila;

28. ndi Obali, ndi Abimaele, ndi Sheva;

29. ndi Ofiri ndi Havila, ndi obabi; onse amenewa ndi ana a okitani.

30. Kwao kunayamba pa Mesa pakunka ku Sefere phiri la kum'mawa.

31. Amenewa ndi ana a Semu, monga mwa mabanja ao, mwa zinenedwe zao, m'maiko ao, m'mitundu yao.

Genesis 10