Genesis 10:20-23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

20. Amenewa ndi ana amuna a Hamu monga mwa mabanja ao, mwa zinenedwe zao, m'maiko ao, m'mitundu yao.

21. Ndiponso kwa Semu atate wa ana onse a Ebere, mkuru wa Yafeti, kwa iye kunabadwa ana.

22. Ana amuna a Semu; Elamu, ndi Ashuri, ndi Aripakasadi, ndi Ludi, ndi Aramu.

23. Ndi ana a Aramu: Uzi ndi Huli, ndi Getere, ndi Masi.

Genesis 10