Genesis 1:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaziona Mulungu zonse zimene adazipanga, ndipo, taonani, zinali zabwino ndithu. Ndipo panali madzulo ndipo panali m'mawa, tsiku lacisanu ndi cimodzi.

Genesis 1

Genesis 1:22-31