Genesis 1:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mulungu ndipo anati, Dziko lapansi limere maudzu, therere lobala mbeu, ndi mtengo wazipatso wakubala zipatso monga mwa mtundu wace, momwemo muli mbeu yace, pa dziko lapansi: ndipo kunatero.

Genesis 1

Genesis 1:4-17