Filemoni 1:23-25 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Epafra wandende mnzanga mwa Kristu Yesu akulankhula iwe; ateronso, Marko, Aristarko, Dema, Luka, anchito anzanga