Ezekieli 7:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo diso langa silidzakulekerera, sindidzacita cifundo, koma ndidzakubwezera njira zako, ndi zonyansa zako zidzakhala pakati pako; ndipo mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova.

Ezekieli 7

Ezekieli 7:1-12