Ezekieli 7:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ciwawa cauka cikhale ndodo ya coipa; sadzawatsalira ndi mmodzi yense, kapena wa unyinji wao, kapena wa cuma cao; sipadzakhalanso kuwalira maliro.

Ezekieli 7

Ezekieli 7:8-13