Ezekieli 6:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova, pokhala ophedwa ao pakati pa mafano ao, pozinga maguwa ao a nsembe, pa zitunda zonse zazitali, pamwamba pa mapiri onse, ndi patsinde pa mitengo yogudira yonse, ndi patsinde pa thundu ali yense wagudugudu, pomwe adapereka zonunkhira zokoma kwa mafano ao onse.

Ezekieli 6

Ezekieli 6:8-14