Ezekieli 5:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nutengekonso pa amenewa ndi kuwaponya pakati pa moto, ndi kuwatentha m'moto; kucokera kumeneko udzaturuka moto pa nyumba yonse ya Israyeli.

Ezekieli 5

Ezekieli 5:1-12