Ezekieli 5:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace atate adzadya ana pakati pako, ndi ana adzadya atate ao; ndipo ndidzacita maweruzo mwa iwe, ndi akutsala onse ndidzawabalalitsa ku mphepo zonse.

Ezekieli 5

Ezekieli 5:6-16