Ezekieli 48:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kuyambira tsono dziko la Alevi kufikira dziko la mudzi, ndiwo a pakati pa magawo ace a kalonga, pakati pa malire a Yuda ndi malire a Benjamini, kukhale kwa kalonga.

Ezekieli 48

Ezekieli 48:18-23