Ezekieli 48:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mudziwo ukhale ndi busa lace; kumpoto mabango mazana awiri mphambu makumi asanu, kumwela mazana awiri mphambu makumi asanu, ndi kum'mawa mazana awiri mphambu makumi asanu, ndi kumadzulo mazana awiri mphambu makumi asanu.

Ezekieli 48

Ezekieli 48:9-21