Ezekieli 48:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo zikwi zisanu zotsalazo m'kupingasa kwace, cakuno ca zikwi makumi awiri mphambu zisanu, zikhale za nchito wamba za mudzi, za kumangapo zapabusa; ndi mudzi ukhale pakati pace.

Ezekieli 48

Ezekieli 48:14-18