Ezekieli 48:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cidzakhala ca ansembe opatulidwa a ana a Zadoki, amene anasunga udikiro wanga osasokera, muja anasokera ana a Israyeli, ndi muja anasokera Alevi.

Ezekieli 48

Ezekieli 48:6-14