Ezekieli 47:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo malire a dzikoli ndi awa: mbali ya kumpoto, kuyambira ku nyanja yaikuru, kutsata njira ya ku Heteloni, kufikira polowera ku Zedadi;

Ezekieli 47

Ezekieli 47:6-23