Ezekieli 47:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Ambuye Yehova, Malire amene mugawe nao dziko likhale colowa cao monga mwa mafuko khumi ndi awiri a Israyeli ndi awa: Yosefe akhale nao magawo awiri.

Ezekieli 47

Ezekieli 47:10-17