Ezekieli 46:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo nsembe ya tsiku lokhala mwezi ikhale mwana wa ng'ombe wopanda cirema, ndi ana a nkhosa asanu ndi mmodzi, ndi nkhosa yamphongo, zikhale zopanda cirema;

Ezekieli 46

Ezekieli 46:5-8