Ezekieli 46:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Uziperekanso kwa Yehova mwana wa nkhosa wa caka cimodzi akhale nsembe yopsereza wopanda cirema, tsiku ndi tsiku, m'mawa ndi m'mawa, uzimpereka.

Ezekieli 46

Ezekieli 46:11-22