Ezekieli 46:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi pamadyerero, ndi pa masiku opatulika, nsembe yaufa ikhale ya efa wa pa ng'ombe, ndi efa wa pa nkhosa yamphongo, ndi pa ana a nkhosa, monga akhoza kupatsa; ndi hini wa mafuta wa paefa.

Ezekieli 46

Ezekieli 46:7-21