Ezekieli 45:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo wansembe atengeko mwazi wa nsembe yaucimo, naupake pa mphuthu za kacisi, ndi pa ngondya zinai za phaka la guwa la nsembe, ndi pa mphuthu za cipata ca bwalo lam'kati.

Ezekieli 45

Ezekieli 45:18-23