Ezekieli 43:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Masiku asanu ndi awiri uzikonzera mbuzi tsiku ndi tsiku, ikhale nsembe yaucimo; akonzerenso mwana wa ng'ombe, ndi nkhosa yamphongo ya zoweta zopanda cirema.

Ezekieli 43

Ezekieli 43:15-27